" Freely you have received, freely give " (Matthew 10:8)

HOME  |  SITEMAP  |  CONTACT US  |  HELP    
Bible Studies Free Christian Books Free Christian eBooks About Us
  Free eBook Version of Chichewa edition 15

 


Paul C. Jongís Kukula Mumzimu Mundandanda wa 4:

- Kalata Woyamba wa Yohane (II)

 • Electronic Book Format : Acrobat PDF Reader
 • Current Downloads : 0
 • About this book
 • Table of Contents
 

Kulengeza:

Paul C. Jong's Kukula Mumzimu Mundandanda wa 4: Kalata Woyamba wa Yohane (II)

Kufothokoza:

Ngati ndiwe Mkristu woona, ufunika kudziwa chikondi cha kwambiri koposa mwa ziphunzitso chabe. Onse amene odziwa ndi kukhulupilira Yesu ngati Mípulumutsi wawo ayenera kudziwa chikondi cha Mulungu mwathunthu mu chikhululukiro chawo cha machimo cimene chinakwanilitsidwa kupitira mu Mawu a uthenga wa madzi ndi Mzimu. Tiyenera kukhala okhulupilira oona mu uthengawu oona kotero kuti tidziwe chikondi cha Mulungu mozama. Mu uthengau oona, chikondi cha Mulungu chikuvumbulutsidwa mwathunthu ndiponso mozama. Ngati tikufuna kudziwa Mulungu ngati chikondi, kuzindikira kwathu kuyenera kuchokera ku chikondi chathunthu cha Mulungu kwa ife cimene chinavumbulutsidwa mu Choonadi cha uthenga wa madzi ndi Mzimu. Ndipokhapo pamene tingatengere anthu ena ku chikondi choona cha Mulungu.
Monga mmene chinalembedwa mu Mawu a Mulungu, madzi akutanthauza ubatizo wa Yesu umene Iye analandira kwa Yohane Míbatizi, ndipo mwazi akutanthauza chiweruzo cimene Iye analandira cifukwa cha machimo athu onse. Ndiponso, umboni wa chipulumutso chathu ukugona mu Mzimu Woyera, madzi, ndi mwazi (1 Yohane 5:8). Mautumiki a madzi, mwazi, ndi Mzimu Woyera ndi aja a Mulungu kupitira mu ameneo Iye anaombora ochimwa kumachimo awo onse.


Mau a wosindikiza:

Chinthu chofunikira kuti ife tidziwe ndi kuti Yesu analandira ubatizo kwa Yohane Míbatizi mu Mtsinje wa Yorodano kotero kuti Iye anyamure machimo adziko pa Iyeyekha Iye asanapachikidwe pa Mtanda. Koma, bvuto lalikulu ndi lakuti anthu ambiri sakudziwa za choonacho. Chotero, tiyenera kugwiririra nji kuti ubatizo wa Yesu kunali kunyamula machimo adzikoli pa Iyeyekha mwa kamodzi Iye asanapachikidwe pa Mtanda. Kudziwa ndi kukhulupilira mwa Yesu Khristu ngati Mípulumutsi wathu, amene anabwera mdziko kudzera mwa uthenga wa madzi ndi Mzimu, ndi chofunikira kwambiri pakuchotsa machimo athu onse.


 

 
Free Christian eBooks
    eBook List
    Chichewa edition 15
 
 • About this book
 •  
 • Table of Contents
 •     What is eBook?
   
 • About eBook
 •  
 • How to read an eBook?
 •  
 • FAQ
 •  
 • Download Help
 •     eBook Readers
   
 • MS Reader 2.0
 •  
 • Acrobat Reader 4.0
 •  

  register as a coworker
  Partner's Zone
     
  Copyright © 2001 - 2018 The New Life Mission. All Rights Reserved.